-
Oweruza 6:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Atatero, mngelo wa Yehova anatambasula dzanja lake, ndipo anakhudza nyama ndi mikate yopanda chofufumitsayo ndi nsonga ya ndodo imene inali m’dzanja lake. Pamenepo, moto wotuluka m’mwalawo unayamba kulilima, n’kunyeketsa nyama ndi mkate wopanda chofufumitsawo,+ koma mngelo wa Yehova anazimiririka.
-