2 Samueli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno ana atatu aamuna a Zeruya,+ amene ndi Yowabu,+ Abisai,+ ndi Asaheli+ anali pamenepo. Asaheli anali waliwiro kwambiri ngati mbawala+ yothamanga m’thengo. 2 Samueli 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Abisai,+ m’bale wake wa Yowabu mwana wa Zeruya+ anali mtsogoleri wa anthu 30 amenewo. Iye ananyamula mkondo ndi kupha nawo anthu 300. Abisai anali wotchuka ngati amuna atatu aja.+ 1 Mbiri 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Alongo awo anali Zeruya ndi Abigayeli,+ ndipo Zeruya anali ndi ana atatu: Abisai,+ Yowabu,+ ndi Asaheli.+
18 Ndiyeno ana atatu aamuna a Zeruya,+ amene ndi Yowabu,+ Abisai,+ ndi Asaheli+ anali pamenepo. Asaheli anali waliwiro kwambiri ngati mbawala+ yothamanga m’thengo.
18 Koma Abisai,+ m’bale wake wa Yowabu mwana wa Zeruya+ anali mtsogoleri wa anthu 30 amenewo. Iye ananyamula mkondo ndi kupha nawo anthu 300. Abisai anali wotchuka ngati amuna atatu aja.+
16 Alongo awo anali Zeruya ndi Abigayeli,+ ndipo Zeruya anali ndi ana atatu: Abisai,+ Yowabu,+ ndi Asaheli.+