Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Davide atamva zimenezi anatumiza Yowabu ndi gulu lonse lankhondo pamodzi ndi amuna amphamvu.+

  • 2 Samueli 18:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Atatero, Davide anagawa anthuwo m’magulu atatu.+ Gulu loyamba analipereka kwa Yowabu,+ gulu lachiwiri analipereka kwa Abisai+ mwana wa Zeruya, m’bale wake wa Yowabu,+ ndipo gulu lachitatu analipereka kwa Itai+ Mgiti. Kenako mfumu inauza anthuwo kuti: “Inenso ndipita nanu sindilephera.”

  • 2 Samueli 24:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho mfumu inauza Yowabu+ mkulu wa magulu ankhondo amene anali naye kuti: “Yendayenda m’mafuko onse a Isiraeli kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba.+ Ndipo amuna inu muwerenge anthu+ kuti ndidziwe chiwerengero chawo.”+

  • 1 Mafumu 11:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pa nthawi imene Davide anawononga Edomu,+ Yowabu, mkulu wa asilikali, anapita kukafotsera anthu amene anaphedwa. Kumeneko anayambanso kupha mwamuna aliyense wa ku Edomu.+

  • 1 Mbiri 11:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chotero Davide anati: “Aliyense amene ayambirire kuukira+ Ayebusi akhala mtsogoleri ndiponso kalonga.” Pamenepo Yowabu+ mwana wa Zeruya ndiye anayamba kupita, choncho anakhala mtsogoleri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena