2 Samueli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika. 2 Samueli 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Davide atamva zimenezi anatumiza Yowabu ndi gulu lonse lankhondo pamodzi ndi amuna amphamvu.+
16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.