2 Samueli 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mayina a amuna amphamvu+ a Davide ndi awa: Yosebu-basebete+ Mtahakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake n’kupha anthu 800 ulendo umodzi. 1 Mbiri 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Davide atamva zimenezi, nthawi yomweyo anatumiza Yowabu+ ndi gulu lonse lankhondo pamodzi ndi amuna amphamvu.+
8 Mayina a amuna amphamvu+ a Davide ndi awa: Yosebu-basebete+ Mtahakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake n’kupha anthu 800 ulendo umodzi.
8 Davide atamva zimenezi, nthawi yomweyo anatumiza Yowabu+ ndi gulu lonse lankhondo pamodzi ndi amuna amphamvu.+