1 Mbiri 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Uwu ndiwo mndandanda wa amuna amphamvu a Davide: Yasobeamu+ mwana wa Mhakimoni, yemwe anali mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake n’kupha anthu 300 ulendo umodzi.+ 1 Mbiri 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mtsogoleri wa gulu loyamba, la mwezi woyamba, anali Yasobeamu+ mwana wa Zabidiyeli. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
11 Uwu ndiwo mndandanda wa amuna amphamvu a Davide: Yasobeamu+ mwana wa Mhakimoni, yemwe anali mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake n’kupha anthu 300 ulendo umodzi.+
2 Mtsogoleri wa gulu loyamba, la mwezi woyamba, anali Yasobeamu+ mwana wa Zabidiyeli. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.