2 Samueli 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mayina a amuna amphamvu+ a Davide ndi awa: Yosebu-basebete+ Mtahakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake n’kupha anthu 800 ulendo umodzi. 1 Mbiri 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mtsogoleri wa gulu loyamba, la mwezi woyamba, anali Yasobeamu+ mwana wa Zabidiyeli. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
8 Mayina a amuna amphamvu+ a Davide ndi awa: Yosebu-basebete+ Mtahakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake n’kupha anthu 800 ulendo umodzi.
2 Mtsogoleri wa gulu loyamba, la mwezi woyamba, anali Yasobeamu+ mwana wa Zabidiyeli. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.