8 Mayina a amuna amphamvu+ a Davide ndi awa: Yosebu-basebete+ Mtahakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake n’kupha anthu 800 ulendo umodzi.
11 Uwu ndiwo mndandanda wa amuna amphamvu a Davide: Yasobeamu+ mwana wa Mhakimoni, yemwe anali mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake n’kupha anthu 300 ulendo umodzi.+