Oweruza 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno amuna 300 aja anawagawa m’magulu atatu. Aliyense anamupatsa lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndi mtsuko waukulu wopanda kanthu, ndipo m’mitsukomo anaikamo miyuni. Miyambo 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+
16 Ndiyeno amuna 300 aja anawagawa m’magulu atatu. Aliyense anamupatsa lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndi mtsuko waukulu wopanda kanthu, ndipo m’mitsukomo anaikamo miyuni.
18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+