1 Mbiri 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero Davide anauza Yowabu+ ndi atsogoleri a anthu kuti: “Pitani mukawerenge+ Aisiraeli kuyambira ku Beere-seba+ mpaka ku Dani,+ ndipo mubweretse chiwerengero chawo kwa ine kuti ndidziwe kuchuluka kwawo.”+
2 Chotero Davide anauza Yowabu+ ndi atsogoleri a anthu kuti: “Pitani mukawerenge+ Aisiraeli kuyambira ku Beere-seba+ mpaka ku Dani,+ ndipo mubweretse chiwerengero chawo kwa ine kuti ndidziwe kuchuluka kwawo.”+