1 Mbiri 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Davide anauza Yowabu+ ndi atsogoleri a anthu kuti: “Pitani mukawerenge Aisiraeli kuyambira ku Beere-seba mpaka ku Dani+ ndipo mubweretse lipoti kuti ndidziwe chiwerengero chawo.”
2 Choncho Davide anauza Yowabu+ ndi atsogoleri a anthu kuti: “Pitani mukawerenge Aisiraeli kuyambira ku Beere-seba mpaka ku Dani+ ndipo mubweretse lipoti kuti ndidziwe chiwerengero chawo.”