Oweruza 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuwonjezera apo, anatcha mzindawo kuti Dani, kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani,+ amene anali wobadwa kwa Isiraeli.+ Ngakhale zili choncho, dzina loyamba la mzindawo linali Laisi.+ 2 Samueli 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndi kusamutsa ufumu kuuchotsa m’nyumba ya Sauli, n’kukhazikitsa mpando wachifumu wa Davide mu Isiraeli ndi mu Yuda, kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba.”+
29 Kuwonjezera apo, anatcha mzindawo kuti Dani, kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani,+ amene anali wobadwa kwa Isiraeli.+ Ngakhale zili choncho, dzina loyamba la mzindawo linali Laisi.+
10 ndi kusamutsa ufumu kuuchotsa m’nyumba ya Sauli, n’kukhazikitsa mpando wachifumu wa Davide mu Isiraeli ndi mu Yuda, kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba.”+