Genesis 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zitatero, Rakele anati: “Mulungu wakhala monga woweruza+ wanga ndipo wamvera mawu anga, choncho wandipatsa mwana wamwamuna.” N’chifukwa chake Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Dani.*+ Genesis 32:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako munthuyo anati: “Dzina lako silikhalanso Yakobo, koma Isiraeli,*+ pakuti walimbana+ ndi Mulungu ndi anthu, ndipo potsirizira pake wapambana.”
6 Zitatero, Rakele anati: “Mulungu wakhala monga woweruza+ wanga ndipo wamvera mawu anga, choncho wandipatsa mwana wamwamuna.” N’chifukwa chake Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Dani.*+
28 Kenako munthuyo anati: “Dzina lako silikhalanso Yakobo, koma Isiraeli,*+ pakuti walimbana+ ndi Mulungu ndi anthu, ndipo potsirizira pake wapambana.”