Oweruza 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndipotu ine sindinakuchimwire, koma iwe ukundilakwira pomenyana nane. Yehova amene ndi Woweruza,+ aweruze lero pakati pa ana a Isiraeli ndi ana a Amoni.’” Salimo 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiweruzeni,+ inu Yehova, pakuti ine ndayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika,+Ndipo ndikudalira Yehova kuti ndisagwedezeke.+ Salimo 75:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ndiye woweruza.+Amatsitsa wina ndi kukweza wina.+
27 Ndipotu ine sindinakuchimwire, koma iwe ukundilakwira pomenyana nane. Yehova amene ndi Woweruza,+ aweruze lero pakati pa ana a Isiraeli ndi ana a Amoni.’”
26 Ndiweruzeni,+ inu Yehova, pakuti ine ndayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika,+Ndipo ndikudalira Yehova kuti ndisagwedezeke.+