2 Mafumu 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+ Miyambo 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu wolungama amayenda ndi mtima wosagawanika,+ ndipo ana ake amakhala odala.+
3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+