-
1 Mafumu 3:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Solomo atamva anati: “Inu mwasonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa mtumiki wanu Davide bambo anga, popeza anayenda pamaso panu m’choonadi ndi m’chilungamo+ ndiponso anali wowongoka mtima pamaso panu. Munapitiriza kumusonyeza kukoma mtima kosatha kumeneku moti munam’patsa mwana kuti lero akhale pampando wake wachifumu.+
-