Salimo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,+ amene amachita chilungamo,+Ndi kulankhula zoona mumtima mwake.+ Salimo 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzakhalabe wopanda cholakwa pamaso pake,+Ndipo ndidzayesetsa kupewa kuchita cholakwa.+
2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,+ amene amachita chilungamo,+Ndi kulankhula zoona mumtima mwake.+