Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 3:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Pakuti munthu wochita zachiphamaso+ Yehova amanyansidwa naye,+ koma amakonda anthu owongoka mtima.+

  • Miyambo 12:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mlomo wa choonadi+ ndi umene udzakhazikike kwamuyaya,+ koma lilime lachinyengo lidzangokhalapo kwa kanthawi.+

  • Zekariya 8:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘Anthu inu muzichita zinthu izi:+ Muzilankhulana zoona zokhazokha.+ Poweruza milandu m’zipata za mizinda yanu, muziweruza mogwirizana ndi choonadi komanso molimbikitsa mtendere.+

  • Aefeso 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+

  • Akolose 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Musamanamizane.+ Vulani umunthu+ wakale pamodzi ndi ntchito zake,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena