Yesaya 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzaweruza mwachilungamo anthu onyozeka+ ndipo adzadzudzula anthu mowongoka mtima, pothandiza ofatsa a padziko lapansi. Adzakwapula dziko lapansi ndi ndodo ya pakamwa pake,+ ndipo adzagwiritsa ntchito mzimu wa pakamwa pake kupha munthu woipa.+ Amosi 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Danani ndi choipa ndipo muzikonda chabwino.+ Chitani zinthu zachilungamo pachipata cha mzinda,+ mwina Yehova Mulungu wa makamu adzakomera mtima+ otsala a Yosefe.’+ Zekariya 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Muzichita chilungamo chenicheni poweruza milandu.+ Muzisonyezana kukoma mtima kosatha+ ndi chifundo.+
4 Adzaweruza mwachilungamo anthu onyozeka+ ndipo adzadzudzula anthu mowongoka mtima, pothandiza ofatsa a padziko lapansi. Adzakwapula dziko lapansi ndi ndodo ya pakamwa pake,+ ndipo adzagwiritsa ntchito mzimu wa pakamwa pake kupha munthu woipa.+
15 Danani ndi choipa ndipo muzikonda chabwino.+ Chitani zinthu zachilungamo pachipata cha mzinda,+ mwina Yehova Mulungu wa makamu adzakomera mtima+ otsala a Yosefe.’+
9 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Muzichita chilungamo chenicheni poweruza milandu.+ Muzisonyezana kukoma mtima kosatha+ ndi chifundo.+