Salimo 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Yehova ndi wolungama.+ Amakonda ntchito zolungama.+Anthu owongoka mtima ndi amene adzaona nkhope yake.+
7 Pakuti Yehova ndi wolungama.+ Amakonda ntchito zolungama.+Anthu owongoka mtima ndi amene adzaona nkhope yake.+