Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 19:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Gawo la ana a Dani linawachepera,+ choncho anapita kukachita nkhondo ku Lesemu.+ Analanda mzindawo n’kupha anthu ake ndi lupanga. Kenako anautenga n’kuyamba kukhalamo ndipo anautcha Lesemu Dani, potengera dzina la kholo lawo Dani.+

  • Oweruza 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho amuna asanu aja anapitiriza ulendo wawo ndipo anafika kumzinda wa Laisi.+ Kumeneko anaona kuti anthu a mumzindawo anali kukhala mosadalira aliyense, malinga ndi chikhalidwe cha Asidoni. Iwo anali kukhala phee, mosatekeseka,+ ndipo panalibe amene anawagonjetsa n’kumawachitira nkhanza kapena kuwavutitsa m’dzikolo. Kuwonjezera apo, anali kukhala kutali kwambiri ndi Asidoni+ ndipo sanali kuyenderana ndi anthu a m’madera ena.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena