2 Samueli 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako mfumu inauza Itai+ Mgiti kuti: “Kodi iweyo ukupita nafe chifukwa chiyani? Bwerera+ ukakhale ndi mfumu, pakuti ndiwe mlendo komanso ndiwe wothawa kwanu. 2 Samueli 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma Itai anayankha mfumu kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo, komanso pali moyo wanu mbuyanga mfumu,+ kulikonse kumene inu mbuyanga mfumu mudzapita ine mtumiki wanu ndidzapitanso komweko, ndipo ndili wokonzeka ngakhale kufa nanu limodzi!”+
19 Kenako mfumu inauza Itai+ Mgiti kuti: “Kodi iweyo ukupita nafe chifukwa chiyani? Bwerera+ ukakhale ndi mfumu, pakuti ndiwe mlendo komanso ndiwe wothawa kwanu.
21 Koma Itai anayankha mfumu kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo, komanso pali moyo wanu mbuyanga mfumu,+ kulikonse kumene inu mbuyanga mfumu mudzapita ine mtumiki wanu ndidzapitanso komweko, ndipo ndili wokonzeka ngakhale kufa nanu limodzi!”+