Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 3:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ine lero ndafooka ngakhale kuti ndine mfumu yodzozedwa,+ ndipo ine ndikuona kuti amuna awa, ana a Zeruya,+ achita nkhanza kwambiri.+ Yehova abwezere aliyense wochita zinthu zoipa mogwirizana ndi kuipa kwake.”+

  • 2 Samueli 8:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.

  • 2 Samueli 20:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma Amasa sanachenjere ndi lupanga limene linali m’manja mwa Yowabu. Choncho Yowabuyo anamubaya+ nalo m’mimba ndipo matumbo ake anakhuthukira pansi, moti sanachite kumubaya kawiri. Chotero Amasa anafa. Pamenepo Yowabu ndi Abisai m’bale wake anathamangitsa Sheba mwana wa Bikiri.

  • 1 Mbiri 11:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chotero Davide anati: “Aliyense amene ayambirire kuukira+ Ayebusi akhala mtsogoleri ndiponso kalonga.” Pamenepo Yowabu+ mwana wa Zeruya ndiye anayamba kupita, choncho anakhala mtsogoleri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena