2 Samueli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno ana atatu aamuna a Zeruya,+ amene ndi Yowabu,+ Abisai,+ ndi Asaheli+ anali pamenepo. Asaheli anali waliwiro kwambiri ngati mbawala+ yothamanga m’thengo. 2 Samueli 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yowabu ndi m’bale wake Abisai,+ anapha Abineri+ chifukwa chakuti iye anapha Asaheli m’bale wawo pa nkhondo ku Gibeoni.+ 2 Samueli 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Asaheli+ m’bale wake wa Yowabu anali m’gulu la amuna 30 aja. M’gululi munalinso Elihanani+ mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,
18 Ndiyeno ana atatu aamuna a Zeruya,+ amene ndi Yowabu,+ Abisai,+ ndi Asaheli+ anali pamenepo. Asaheli anali waliwiro kwambiri ngati mbawala+ yothamanga m’thengo.
30 Yowabu ndi m’bale wake Abisai,+ anapha Abineri+ chifukwa chakuti iye anapha Asaheli m’bale wawo pa nkhondo ku Gibeoni.+
24 Asaheli+ m’bale wake wa Yowabu anali m’gulu la amuna 30 aja. M’gululi munalinso Elihanani+ mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,