2 Samueli 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zitatero, Yowabu ndi Abisai anathamangitsa Abineri. Pamene dzuwa linali kulowa, iwo anafika paphiri la Ama, limene lili pafupi ndi Giya panjira yopita kuchipululu cha Gibeoni.+
24 Zitatero, Yowabu ndi Abisai anathamangitsa Abineri. Pamene dzuwa linali kulowa, iwo anafika paphiri la Ama, limene lili pafupi ndi Giya panjira yopita kuchipululu cha Gibeoni.+