Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “‘Usabwezere choipa+ kapena kusungira chakukhosi anthu amtundu wako.+ Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.+ Ine ndine Yehova.

  • 2 Samueli 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma Asaheli anakanabe kutembenukira kwina. Choncho Abineri anamubaya* pamimba+ ndi chogwirira cha mkondo, ndipo mkondowo unatulukira kumsana kwake, moti anagwa pansi n’kufera pomwepo. Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, aliyense wofika pamalo amene Asaheli anagwera ndi kufa, anali kuima chilili+ ndi kudabwa kwambiri.

  • Aroma 12:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Okondedwa, musabwezere choipa,+ koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Pakuti Malemba amati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine, watero Yehova.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena