Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiyeno ana atatu aamuna a Zeruya,+ amene ndi Yowabu,+ Abisai,+ ndi Asaheli+ anali pamenepo. Asaheli anali waliwiro kwambiri ngati mbawala+ yothamanga m’thengo.

  • 2 Samueli 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma Asaheli anakanabe kutembenukira kwina. Choncho Abineri anamubaya* pamimba+ ndi chogwirira cha mkondo, ndipo mkondowo unatulukira kumsana kwake, moti anagwa pansi n’kufera pomwepo. Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, aliyense wofika pamalo amene Asaheli anagwera ndi kufa, anali kuima chilili+ ndi kudabwa kwambiri.

  • 1 Mbiri 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Alongo awo anali Zeruya ndi Abigayeli,+ ndipo Zeruya anali ndi ana atatu: Abisai,+ Yowabu,+ ndi Asaheli.+

  • 1 Mbiri 27:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mtsogoleri wachinayi, wa mwezi wachinayi, anali Asaheli+ m’bale wake wa Yowabu,+ ndipo mwana wake Zebadiya anabwera pambuyo pake. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena