2 Samueli 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu ena onse anawapereka kwa mchimwene wake Abisai+ kuti awatsogolere pokamenyana ndi Aamoni.+