Genesis 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero. Numeri 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+ 1 Mbiri 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu ena onse anawapereka m’manja mwa Abisai+ m’bale wake, kuti afole mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi kukumana ndi ana a Amoni.+
38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero.
24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+
11 Anthu ena onse anawapereka m’manja mwa Abisai+ m’bale wake, kuti afole mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi kukumana ndi ana a Amoni.+