2 Samueli 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nthawi yomweyo Abisai+ mwana wa Zeruya anathandiza+ Davide ndipo anakantha Mfilisitiyo ndi kumupha. Pamenepo asilikali a Davide analumbira kwa iye kuti: “Simudzapitanso ndi ife kunkhondo,+ chifukwa mungazimitse+ nyale+ ya Isiraeli!” 1 Mbiri 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Alongo awo anali Zeruya ndi Abigayeli,+ ndipo Zeruya anali ndi ana atatu: Abisai,+ Yowabu,+ ndi Asaheli.+
17 Nthawi yomweyo Abisai+ mwana wa Zeruya anathandiza+ Davide ndipo anakantha Mfilisitiyo ndi kumupha. Pamenepo asilikali a Davide analumbira kwa iye kuti: “Simudzapitanso ndi ife kunkhondo,+ chifukwa mungazimitse+ nyale+ ya Isiraeli!”
16 Alongo awo anali Zeruya ndi Abigayeli,+ ndipo Zeruya anali ndi ana atatu: Abisai,+ Yowabu,+ ndi Asaheli.+