Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 26:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Davide anauza Ahimeleki Mhiti+ ndi Abisai+ mwana wa Zeruya,+ m’bale wake wa Yowabu, kuti: “Ndani atsike nane kupita kwa Sauli kumsasa?” Abisai anayankha kuti: “Ine ndipita nawe.”+

  • 2 Samueli 3:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Yowabu ndi m’bale wake Abisai,+ anapha Abineri+ chifukwa chakuti iye anapha Asaheli m’bale wawo pa nkhondo ku Gibeoni.+

  • 2 Samueli 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Anthu ena onse anawapereka m’manja mwa Abisai+ m’bale wake, kuti awatsogolere pofola mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi kukumana ndi ana a Amoni.+

  • 2 Samueli 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Davide anauza Abisai+ kuti: “Tsopano Sheba+ mwana wamwamuna wa Bikiri atisautsa kwambiri kuposa Abisalomu.+ Iweyo utenge atumiki+ a mbuye wako ndi kumuthamangitsa kuti asapeze mizinda ya mipanda yolimba kwambiri ndi kutizemba ife tikuona.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena