2 Samueli 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anauza Abisai kuti:+ “Sheba+ mwana wamwamuna wa Bikiri ativutitsa kwambiri kuposa Abisalomu.+ Ndiye utenge atumiki a mbuye wako ndipo mukamusake kuti asapeze mizinda ya mipanda yolimba kwambiri nʼkubisala.”
6 Ndiyeno Davide anauza Abisai kuti:+ “Sheba+ mwana wamwamuna wa Bikiri ativutitsa kwambiri kuposa Abisalomu.+ Ndiye utenge atumiki a mbuye wako ndipo mukamusake kuti asapeze mizinda ya mipanda yolimba kwambiri nʼkubisala.”