1 Samueli 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anauza Ahimeleki Muhiti+ ndi Abisai+ mwana wa Zeruya,+ mchimwene wake wa Yowabu, kuti: “Ndani apite nane kwa Sauli kumsasa?” Abisai anayankha kuti: “Ine ndipita nanu.” 2 Samueli 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu ena onse anawapereka kwa mchimwene wake Abisai+ kuti awatsogolere pokamenyana ndi Aamoni.+ 2 Samueli 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Abisai,+ mchimwene wake wa Yowabu mwana wa Zeruya+ anali mtsogoleri wa anthu ena atatu. Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 300. Abisai anali wotchuka ngati amuna atatu aja.+ 1 Mbiri 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Abisai+ mwana wa Zeruya,+ anapha Aedomu 18,000 mʼchigwa cha Mchere.+
6 Ndiyeno Davide anauza Ahimeleki Muhiti+ ndi Abisai+ mwana wa Zeruya,+ mchimwene wake wa Yowabu, kuti: “Ndani apite nane kwa Sauli kumsasa?” Abisai anayankha kuti: “Ine ndipita nanu.”
18 Abisai,+ mchimwene wake wa Yowabu mwana wa Zeruya+ anali mtsogoleri wa anthu ena atatu. Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 300. Abisai anali wotchuka ngati amuna atatu aja.+