Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 21:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndiyeno Ahabu anafunsa Eliya kuti: “Wandipeza kodi mdani wanga?”+ Eliya anayankha kuti: “Inde ndakupezani. ‘Popeza watsimikiza mtima kuti uchite zoipa pamaso pa Yehova,+

  • 2 Mbiri 25:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mneneriyo atangonena zimenezi, mfumuyo inamufunsa kuti: “Kodi tinakuika kuti ukhale mlangizi wa mfumu?+ Siya kunena zimenezi.+ Kodi ukufuna kuti akuphe?” Choncho mneneriyo anasiya, koma anati: “Ndithu ndikudziwa kuti Mulungu watsimikiza kuti akuwonongeni+ chifukwa cha zimene mwachitazi,+ ndiponso chifukwa simunamvere malangizo anga.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena