Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Amene amalangiza wonyoza amadzichotsera yekha ulemu,+ ndipo amene amadzudzula woipa amadzibweretsera chilema.+

  • Miyambo 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Munthu wosiya njira yabwino amadana ndi malangizo.+ Aliyense wodana ndi chidzudzulo adzafa.+

  • Yesaya 30:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+

  • 2 Timoteyo 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti idzafika nthawi imene anthu sadzafunanso chiphunzitso cholondola,+ koma mogwirizana ndi zilakolako zawo, adzadzipezera aphunzitsi kuti amve zowakomera m’khutu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena