Levitiko 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Koma mukapitirizabe kuchita zosemphana ndi zofuna zanga, osafuna kundimvera, pamenepo ndidzakukanthani mowirikiza ka 7 malinga ndi machimo anu.+ Miyambo 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pakuti kupanduka+ kwa osadziwa n’kumene kudzawaphe+ ndipo mphwayi za opusa n’zimene zidzawawononge.+ Miyambo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawiyo udzanena kuti: “Ndinkadana ndi malangizo* ine,+ ndipo mtima wanga sunkavomereza kudzudzula.+ Miyambo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amene wagwira malangizo* mwamphamvu ndiye njira ya kumoyo,+ koma wosiya chidzudzulo amasocheretsa anthu.+
21 “‘Koma mukapitirizabe kuchita zosemphana ndi zofuna zanga, osafuna kundimvera, pamenepo ndidzakukanthani mowirikiza ka 7 malinga ndi machimo anu.+
32 Pakuti kupanduka+ kwa osadziwa n’kumene kudzawaphe+ ndipo mphwayi za opusa n’zimene zidzawawononge.+
12 Pa nthawiyo udzanena kuti: “Ndinkadana ndi malangizo* ine,+ ndipo mtima wanga sunkavomereza kudzudzula.+
17 Amene wagwira malangizo* mwamphamvu ndiye njira ya kumoyo,+ koma wosiya chidzudzulo amasocheretsa anthu.+