Miyambo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawiyo udzanena kuti: “Ndinkadana ndi malangizo* ine,+ ndipo mtima wanga sunkavomereza kudzudzula.+ Miyambo 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wosiya njira yabwino amadana ndi malangizo.+ Aliyense wodana ndi chidzudzulo adzafa.+ 2 Timoteyo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo adzasiya kumvetsera choonadi, n’kutembenukira ku nkhani zonama.+ Aheberi 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Samalani kuti musasiye kumvetsera wolankhulayo.+ Pakuti ngati amene analephera kumvera wopereka chenjezo la Mulungu padziko lapansi sanapulumuke,+ kuli bwanji ifeyo? Nafenso sitidzapulumuka tikachoka kwa iye amene amalankhula ali kumwamba.+
12 Pa nthawiyo udzanena kuti: “Ndinkadana ndi malangizo* ine,+ ndipo mtima wanga sunkavomereza kudzudzula.+
25 Samalani kuti musasiye kumvetsera wolankhulayo.+ Pakuti ngati amene analephera kumvera wopereka chenjezo la Mulungu padziko lapansi sanapulumuke,+ kuli bwanji ifeyo? Nafenso sitidzapulumuka tikachoka kwa iye amene amalankhula ali kumwamba.+