Miyambo 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chilango chimaoneka choipa* kwa munthu amene wasiya njira yabwino,+Koma aliyense amene amadana ndi kudzudzulidwa adzafa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:10 Nsanja ya Olonda,7/1/2006, tsa. 15
10 Chilango chimaoneka choipa* kwa munthu amene wasiya njira yabwino,+Koma aliyense amene amadana ndi kudzudzulidwa adzafa.+