1 Mafumu 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ahabu atangomuona Eliya, anati: “Ndiwe eti! Iwe ndiwe munthu amene wachititsa kuti Isiraeli anyanyalidwe.”+ Amosi 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Anthuwo amadana ndi munthu wowadzudzula pachipata cha mzinda,+ komanso amanyansidwa ndi munthu wowauza chilungamo.+ Agalatiya 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi ndakhala mdani+ wanu tsopano chifukwa ndakuuzani zoona?+
17 Ahabu atangomuona Eliya, anati: “Ndiwe eti! Iwe ndiwe munthu amene wachititsa kuti Isiraeli anyanyalidwe.”+
10 “‘Anthuwo amadana ndi munthu wowadzudzula pachipata cha mzinda,+ komanso amanyansidwa ndi munthu wowauza chilungamo.+