1 Mbiri 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 wachitatu Abisalomu,+ wobadwa kwa Maaka+ mwana wamkazi wa Talimai+ mfumu ya Gesuri,+ wachinayi Adoniya,+ wobadwa kwa Hagiti,+ 1 Mbiri 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ku Yerusalemu+ iye anabereka ana awa: Simeya,+ Sobabu,+ Natani,+ ndi Solomo,+ ana anayi obadwa kwa Bati-seba+ mwana wamkazi wa Amiyeli.+
2 wachitatu Abisalomu,+ wobadwa kwa Maaka+ mwana wamkazi wa Talimai+ mfumu ya Gesuri,+ wachinayi Adoniya,+ wobadwa kwa Hagiti,+
5 Ku Yerusalemu+ iye anabereka ana awa: Simeya,+ Sobabu,+ Natani,+ ndi Solomo,+ ana anayi obadwa kwa Bati-seba+ mwana wamkazi wa Amiyeli.+