2 Samueli 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno tsiku lina madzulo, Davide anadzuka pabedi lake, n’kupita kukayendayenda padenga*+ la nyumba yachifumu. Ali pamenepo anaona+ mkazi akusamba, ndipo mkaziyo anali wooneka bwino kwambiri.+
2 Ndiyeno tsiku lina madzulo, Davide anadzuka pabedi lake, n’kupita kukayendayenda padenga*+ la nyumba yachifumu. Ali pamenepo anaona+ mkazi akusamba, ndipo mkaziyo anali wooneka bwino kwambiri.+