2 Samueli 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano manja anu alimbe ndipo mukhale amuna olimba mtima,+ chifukwa mbuye wanu Sauli wamwalira ndipo anthu a nyumba ya Yuda adzoza ine kukhala mfumu+ yawo.”
7 Tsopano manja anu alimbe ndipo mukhale amuna olimba mtima,+ chifukwa mbuye wanu Sauli wamwalira ndipo anthu a nyumba ya Yuda adzoza ine kukhala mfumu+ yawo.”