2 Samueli 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chita zinthu mwamphamvu, ndipo tisonyeze kulimba mtima+ chifukwa cha anthu athu, ndiponso chifukwa cha mizinda ya Mulungu wathu.+ Yehova adzachita zimene zili zabwino m’maso mwake.”+
12 Chita zinthu mwamphamvu, ndipo tisonyeze kulimba mtima+ chifukwa cha anthu athu, ndiponso chifukwa cha mizinda ya Mulungu wathu.+ Yehova adzachita zimene zili zabwino m’maso mwake.”+