Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 34:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Yakobo ataona zimenezi anauza Simiyoni ndi Levi+ kuti: “Mwandiputira chidani, ndipo mwandinunkhitsa kwa anthu a m’dziko lino,+ Akanani ndi Aperezi. Ine ndili ndi anthu ochepa,+ ndipo iwowa ndithu asonkhana pamodzi n’kutiukira. Atithira nkhondo n’kutitha tonse, ine ndi banja langa.”

  • 1 Samueli 13:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Isiraeli yense anamva anthu akukamba kuti: “Sauli wakantha mudzi wa asilikali a Afilisiti, ndipo tsopano Isiraeli wakhala chinthu chonunkha+ kwa Afilisiti.” Choncho anasonkhanitsa anthu onse pamodzi kuti atsatire Sauli ku Giligala.+

  • 1 Samueli 27:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Akisi anakhulupirira+ Davide, ndipo mumtima mwake anati: “Mosakayikira, Davide wakhala fungo lonunkha kwa anthu akwawo Aisiraeli,+ ndipo iye akhala mtumiki wanga mpaka kalekale.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena