2 Samueli 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atatero, Davide anaitana mmodzi mwa anyamata ake ndi kumuuza kuti: “Mukanthe.” Chotero anamukanthadi, moti anafa.+ Salimo 55:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipa kumanda.+Ndipo anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso anthu achinyengo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+Koma ine ndidzakhulupirira inu.+
15 Atatero, Davide anaitana mmodzi mwa anyamata ake ndi kumuuza kuti: “Mukanthe.” Chotero anamukanthadi, moti anafa.+
23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipa kumanda.+Ndipo anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso anthu achinyengo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+Koma ine ndidzakhulupirira inu.+