2 Samueli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 pamene munthu wina anandibweretsera uthenga+ wakuti, ‘Sauli wafa,’ ndipo iye anali kuganiza kuti wabweretsa uthenga wabwino, ine ndinamugwira ndi kumupha+ ku Zikilaga m’malo momulipira monga mthenga. 1 Mafumu 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nthawi yomweyo Mfumu Solomo inatumiza lamulo kudzera mwa Benaya+ mwana wa Yehoyada. Iye anapita kukakantha Adoniya, n’kumupha.+
10 pamene munthu wina anandibweretsera uthenga+ wakuti, ‘Sauli wafa,’ ndipo iye anali kuganiza kuti wabweretsa uthenga wabwino, ine ndinamugwira ndi kumupha+ ku Zikilaga m’malo momulipira monga mthenga.
25 Nthawi yomweyo Mfumu Solomo inatumiza lamulo kudzera mwa Benaya+ mwana wa Yehoyada. Iye anapita kukakantha Adoniya, n’kumupha.+