1 Mafumu 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako Benaya mwana wa Yehoyada anapita+ kuchihemako n’kukakantha Yowabu ndi kumupha,+ ndipo anaikidwa m’manda panyumba pake m’chipululu.
34 Kenako Benaya mwana wa Yehoyada anapita+ kuchihemako n’kukakantha Yowabu ndi kumupha,+ ndipo anaikidwa m’manda panyumba pake m’chipululu.