1 Mbiri 6:80 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Kuchokera ku fuko la Gadi,+ anawapatsa mzinda wa Ramoti+ ku Giliyadi ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Mahanaimu+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
80 Kuchokera ku fuko la Gadi,+ anawapatsa mzinda wa Ramoti+ ku Giliyadi ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Mahanaimu+ ndi malo ake odyetserako ziweto,