Genesis 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yakobo atangowaona, anati: “Ilitu ndi gulu la Mulungu!”+ Chotero malowo anawatcha kuti Mahanaimu.*+ 2 Samueli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+ 2 Samueli 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Barizilai anali wokalamba kwambiri pakuti anali ndi zaka 80.+ Pamene mfumu inali kukhala ku Mahanaimu,+ Barizilai anali kuipatsa chakudya pakuti iye anali munthu wolemera kwambiri.+
2 Yakobo atangowaona, anati: “Ilitu ndi gulu la Mulungu!”+ Chotero malowo anawatcha kuti Mahanaimu.*+
8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+
32 Barizilai anali wokalamba kwambiri pakuti anali ndi zaka 80.+ Pamene mfumu inali kukhala ku Mahanaimu,+ Barizilai anali kuipatsa chakudya pakuti iye anali munthu wolemera kwambiri.+