1 Samueli 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma mukachita zinthu zoipa mouma khosi, mudzasesedwa,+ inu pamodzi ndi mfumu yanuyo.”+ 1 Samueli 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno masiku amenewo zinachitika kuti Afilisiti anayamba kusonkhanitsa asilikali awo kuti akamenyane ndi Isiraeli.+ Choncho, Akisi anauza Davide kuti: “Ndikukhulupirira kuti ukudziwa kuti iwe ndi anthu ako muyenera kupita ndi ine kunkhondo.”+ 1 Samueli 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano Afilisiti anali kumenyana ndi Isiraeli,+ ndipo amuna a Isiraeli anathawa pamaso pa Afilisiti, moti anali kuphedwa+ m’phiri la Giliboa.+
28 Ndiyeno masiku amenewo zinachitika kuti Afilisiti anayamba kusonkhanitsa asilikali awo kuti akamenyane ndi Isiraeli.+ Choncho, Akisi anauza Davide kuti: “Ndikukhulupirira kuti ukudziwa kuti iwe ndi anthu ako muyenera kupita ndi ine kunkhondo.”+
31 Tsopano Afilisiti anali kumenyana ndi Isiraeli,+ ndipo amuna a Isiraeli anathawa pamaso pa Afilisiti, moti anali kuphedwa+ m’phiri la Giliboa.+